Ngamila yanga ili kuti? [x8]
Umafuna nthawi zonse, uvutike moyo wonse
Kufuna zonse zabwino, zikhale zako
Ufunefune bwanji, sungalikwanitse dzikoli
Mapeto ake ndikunenetsa udzagonje ndiwe
You search all your life
Stealing all you find
And you stare at your own hands
Not the hands they entwine
Pokuti upeze chuma, mpakana kukhwima
Kunzunitsa mzi..., kuwataya ku moto
Kufunsafunsa mudzi, Ngamila yanga ili kuti?
Chonsecho wakwera ngati wachitila dala
[Baaba Maal]
Pokuti upeze chuma, mpakana kukhwima
Kunzunitsa mzi..., kuwataya ku moto
Kufunsafunsa mudzi, Ngamila yanga ili kuti?
Chonsecho wakwera ngati wachitila dala
You have all you need
When you're held by me
Don't pine for what's not
And whatever will be
You have all you need
When you're held by me
Don't pine for what's not
And whatever will be
Ngamila yanga ili kuti? [x8]